Islamic Sources Other Language

 1. home

 2. book

 3. Mapemphero NdiMakwelero A Munthu Okhulupilira

Mapemphero NdiMakwelero A Munthu Okhulupilira

ALSALAT-MERAJ-ALMOEMEN-28.11

 • Mustapha Qasir
 • 1
 • 978-964-529-843-0
download

  Download

Mapemphero NdiMakwelero A Munthu Okhulupilira
1 (20%) 1 vote[s]
description book specs comment

Ziphunzitso za Ahl al-Bayt (akunyumba kwa Mtumiki -a.s) zomwe zidasungidwa ndi otsatira ake, zilinkusokhanitsa matsamvu amaphunziro onse achipembedzo cha chisilamu. Wakwanitsa mpatuko umenewu kubala anamfuzi apamwamba omwe kuchokera nkutsatira muziphunzitso za akunyumba kwa Mtumuki agwira ntchito yotamandika pakuphunzitsa anthu komanso kuyankha mafunso kuchokera mkati mwachipembedzo cha chisilamu ngakhalenso kunja kwake. Ndipo mukupita kwa zaka zankhaninkhani, apereka anamfuzi amenewa mayankho omveka bwino okhudzana ndi mafunso osiyanasiyana.

 • Mustapha Qasir
 • 1
 • 978-964-529-843-0
 • ABWA Publishing and Printing Center
 • 2016
 • 3000