Islamic Sources Other Language

 1. home

 2. book

 3. Chilungamo Momwe Chilili

Chilungamo Momwe Chilili

Chilungamo Momwe Chilili

 • Ja'far al-Hadi
 • 1
 • Bungwe la dziko lonse la Ahl al-Bayt (‘a)
download

  Download

Chilungamo Momwe Chilili
1 (20%) 1 vote[s]
description book specs comment

Ziphunzitso za Ahl al-Bayt (akunyumba kwa Mtumiki (a.s) zomwe zidasungidwa ndi otsatira ake, zilinkusokhanitsa matsamvu amaphunziro onse achipembedzo cha chisilamu. Wakwanitsa mpatuko umenewu kubala anamfuzi apamwamba omwe kuchokera nkutsatira muziphunzitso za akunyumba kwa Mtumiki agwira ntchito yotamandika pakuphunzitsa anthu komanso kuyankha mafunso kuchokera nkati mwachipembedzo cha chisilamu ngakhalenso kunja kwake. Ndipo mukupita kwa zaka zankhaninkhani, apereka anamfuzi amenewa mayankho omveka bwino okhudzana ndi mafunso osiyanasiyana.

 • Ja'far al-Hadi
 • 1
 • Bungwe la dziko lonse la Ahl al-Bayt (‘a)
 • 2015
 • 1000